Mateyu 16:4 - Buku Lopatulika4 Obadwa oipa ndi achigololo afunafuna chizindikiro; ndipo sadzalandira chizindikiro china, koma chizindikiro cha Yona. Ndipo Iye anawasiya, nachokapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Obadwa oipa ndi achigololo afunafuna chizindikiro; ndipo sadzalandira chizindikiro china, koma chizindikiro cha Yona. Ndipo Iye anawasiya, nachokapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Anthu a mbadwo woipa ndi wosakhulupirika amafuna kuwona chizindikiro chozizwitsa. Komabe sadzaona chizindikiro china kupatula chokha chija cha mneneri Yona.” Atatero, Yesu adaŵasiya nachokapo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mʼbado woyipa ndi wachigololo umafuna chizindikiro chodabwitsa koma palibe ngakhale chimodzi chidzapatsidwa kupatula chizindikiro cha Yona.” Pamenepo Yesu anawasiya nachoka. Onani mutuwo |