Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 1:21 - Buku Lopatulika

21 Potero kuyenera kuti wina wa amunawo anatsatana nafe nthawi yonseyi Ambuye Yesu analowa natuluka mwa ife,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Potero kuyenera kuti wina wa amunawo anatsatana nafe nthawi yonseyi Ambuye Yesu analowa natuluka mwa ife,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 “Pali anthu ena amene akhala akutsagana nafe nthaŵi yonse pamene Ambuye Yesu anali pakati pathu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Chifukwa chake ndi kofunika kusankha mmodzi wa anthu amene akhala nafe nthawi yonse imene Ambuye Yesu ankayenda nafe,

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 1:21
9 Mawu Ofanana  

Masiku anapitawo, pamene Saulo anali mfumu yathu, inu ndinu amene munatsogolera Aisraele kutuluka nao ndi kubwera nao; ndipo Yehova ananena nanu, Uzidyetsa anthu anga Israele, ndi kukhala mtsogoleri wa Israele.


Ndipo tsopano, Yehova Inu Mulungu wanga, mwalonga ine kapolo wanu ufumu m'malo mwa atate wanga Davide, koma ine ndine kamwana, sindidziwa kutuluka kapena kulowa.


wakutuluka pamaso pao, ndi kulowa pamaso pao, wakuwatulutsa ndi kuwalowetsa; kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda mbusa.


monga anazipereka kwa ife iwo amene anakhala mboni ndi atumiki a mau,


Ndipo m'mene analowa sanapeze mtembo wa Ambuye Yesu.


Ndipo inunso muchita umboni, pakuti muli ndi Ine kuyambira chiyambi.


nati nao, Ndine munthu wa zaka zana ndi makumi awiri lero lino; sindikhozanso kutuluka ndi kulowa; ndipo Yehova anati kwa ine, Sudzaoloka Yordani uyu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa