Luka 24:23 - Buku Lopatulika23 ndipo m'mene sanapeze mtembo wake, anadza, nanena kuti adaona m'masomphenya angelo, amene ananena kuti ali ndi moyo Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 ndipo m'mene sanapeze mtembo wake, anadza, nanena kuti adaona m'masomphenya angelo, amene ananena kuti ali ndi moyo Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 ndiye amati sadaupeze mtembo wake. Tsono atabwerako amadzasimba kuti anaona angelo amene anaŵauza kuti Yesu ali moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 koma sanakapeze mtembo wake. Iwo anabwera ndi kudzatiwuza ife kuti anaona masomphenya a angelo amene anati Yesu ali moyo. Onani mutuwo |