Luka 24:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo ena a iwo anali nafe anachoka kunka kumanda, napeza monga momwe akazi adanena; koma Iyeyo sanamuone. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo ena a iwo anali nafe anachoka kunka kumanda, napeza monga momwe akazi adanena; koma Iyeyo sanamuone. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Ena mwa ife anapita kumandako, ndipo anakapezadi monga momwe azimai aja amasimbira, koma Iyeyo sadamuwone ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Kenaka ena mwa anzathu anapita ku manda ndipo anakapeza monga momwe amayiwo ananenera, koma Iye sanamuone.” Onani mutuwo |