Luka 24:22 - Buku Lopatulika22 Komatu akazi enanso a mwa ife anatidabwitsa, ndiwo amene analawirira kumanda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Komatu akazi enanso a mwa ife anatidabwitsa, ndiwo amene analawirira kumanda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Komanso azimai ena a m'gulu lathu anatidabwitsa. Iwowo anapita ku manda m'mamaŵa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Kuwonjezanso apo, ena mwa amayi athu atidabwitsa ife. Iwo anapita ku manda mmamawa Onani mutuwo |