Eksodo 25:7 - Buku Lopatulika miyala yaberulo, ndi miyala yoika paefodi, ndi pachapachifuwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 miyala yaberulo, ndi miyala yoika paefodi, ndi pachapachifuwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ulandirenso miyala yokoma ya onikisi, ndiponso miyala ina yoti uike pa chovala chaunsembe cha efodi, ndi pa chovala chapachifuwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero miyala yokongola ya mtundu wa onikisi ndi ina yabwino yoyika pa efodi ndi pa chovala cha pachifuwa. |
Ndipo zovala azisoka ndi izi: chapachifuwa ndi efodi, ndi mwinjiro, ndi malaya opikapika, ndi nduwira, ndi mpango; tero apangire Aroni mbale wako ndi ana ake zovala zopatulika, kuti andichitire Ine ntchito ya nsembe.
Ndi akulu anabwera nayo miyala yasohamu, ndi miyala yoti aiike kuefodi, ndi kuchapachifuwa;
Ana a maso ake akunga nkhunda pambali pa mitsinje ya madzi; otsukidwa ndi mkaka, okhala pa mitsinje yodzala.