Eksodo 25:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo andimangire malo opatulika; kuti ndikhale pakati pao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo andimangire malo opatulika; kuti ndikhale pakati pao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndipo andipangire chihema chopatulika kuti Ine ndidzakhale pakati pao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Iwo andipangire malo wopatulika, ndipo Ine ndidzakhala pakati pawo. Onani mutuwo |
Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, pano mpokhala mpando wachifumu wanga, mpoponda kumapazi anga, pomwe ndidzakhala pakati pa ana a Israele kosatha; ndi nyumba ya Israele siidzadetsanso dzina langa loyera, ngakhale iwo kapena mafumu ao, mwa chigololo chao, ndi mitembo ya mafumu ao pa misanje yao,