Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 25:7 - Buku Lopatulika

7 miyala yaberulo, ndi miyala yoika paefodi, ndi pachapachifuwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 miyala yaberulo, ndi miyala yoika paefodi, ndi pachapachifuwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ulandirenso miyala yokoma ya onikisi, ndiponso miyala ina yoti uike pa chovala chaunsembe cha efodi, ndi pa chovala chapachifuwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 miyala yokongola ya mtundu wa onikisi ndi ina yabwino yoyika pa efodi ndi pa chovala cha pachifuwa.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 25:7
6 Mawu Ofanana  

golide wa dziko ali wabwino; ndimonso muli bedola ndi mwala wasohamu.


Ndipo zovala azisoka ndi izi: chapachifuwa ndi efodi, ndi mwinjiro, ndi malaya opikapika, ndi nduwira, ndi mpango; tero apangire Aroni mbale wako ndi ana ake zovala zopatulika, kuti andichitire Ine ntchito ya nsembe.


Ndi akulu anabwera nayo miyala yasohamu, ndi miyala yoti aiike kuefodi, ndi kuchapachifuwa;


ndi miyala yasohamu, ndi miyala yoika ya efodi, ndi ya chapachifuwa.


Ana a maso ake akunga nkhunda pambali pa mitsinje ya madzi; otsukidwa ndi mkaka, okhala pa mitsinje yodzala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa