Eksodo 25:9 - Buku Lopatulika9 Monga mwa zonse Ine ndilikuonetsa iwe, chifaniziro cha chihema, ndi chifaniziro cha zipangizo zake zonse, momwemo uchimange. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Monga mwa zonse Ine ndilikuonetsa iwe, chifaniziro cha Kachisi, ndi chifaniziro cha zipangizo zake zonse, momwemo uchimange. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Umange chihemacho monga m'mene ndidzakulangizire mapangidwe ake ndiponso mapangidwe a katundu yense wam'menemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Umange chihema ndiponso ziwiya zamʼkatimo monga momwe Ine ndidzakuonetsere. Onani mutuwo |