Eksodo 25:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo azipanga likasa la mtengo wakasiya: utali wake mikono iwiri ndi hafu, kupingasa kwake mkono ndi hafu, msinkhu wake mkono ndi hafu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo azipanga likasa la mtengo wakasiya: utali wake mikono iwiri ndi hafu, kupingasa kwake mkono ndi hafu, msinkhu wake mkono ndi hafu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 “Ndipo apange bokosi la matabwa a mtengo wa kasiya. Kutalika kwake kukhale masentimita 114, muufupi mwake masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 “Tsono apange bokosi lamatabwa amtengo wa mkesha, ndipo kutalika kwake kukhale masentimita 114, mulifupi mwake masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69. Onani mutuwo |