Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 35:27 - Buku Lopatulika

27 Ndi akulu anabwera nayo miyala yasohamu, ndi miyala yoti aiike kuefodi, ndi kuchapachifuwa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ndi akulu anabwera nayo miyala yasohamu, ndi miyala yoti aiike kuefodi, ndi kuchapachifuwa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Ndipo atsogoleri adabwera ndi miyala ya onikisi ndi miyala ina yoika pa chovala cha efodi ndiponso pa chovala chapachifuwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Atsogoleri anabweretsa miyala ya onikisi ndi miyala yokongola yoyika pa efodi ndi chovala chapachifuwa.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 35:27
6 Mawu Ofanana  

Pamenepo akulu a nyumba za makolo, ndi akulu a mafuko a Israele, ndi akulu a zikwi ndi a mazana pamodzi ndi iwo oyang'anira ntchito ya mfumu, anapereka mwaufulu,


Ndipo akulu ena a nyumba za makolo, pofika kunyumba ya Yehova ili ku Yerusalemu, anapereka chaufulu kwa nyumba ya Mulungu chakuiimika pakuzika pake.


miyala yaberulo, ndi miyala yoika paefodi, ndi pachapachifuwa.


Ndi akazi onse ofulumidwa mtima ndi luso anapota ubweyawo wa mbuzi.


ndi zonunkhira, ndi mafuta akuunikira, ndi mafuta odzoza, ndi chofukiza za fungo lokoma.


ndi miyala yasohamu, ndi miyala yoika ya efodi, ndi ya chapachifuwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa