Eksodo 35:9 - Buku Lopatulika9 ndi miyala yasohamu, ndi miyala yoika ya efodi, ndi ya chapachifuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndi miyala yasohamu, ndi miyala yoika ya efodi, ndi ya chapachifuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 miyala ya mtundu wa onikisi ndi ina yokoma yoika pa chovala chaunsembe cha efodi ndiponso pa chovala chapachifuwa.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 miyala yokongola ya mtundu wa onikisi ndi ina yabwino yoyika pa Efodi ndi pa chovala cha pachifuwa. Onani mutuwo |