Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 35:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo abwere yense wa mtima waluso mwa inu, napange zonse zimene Yehova analamula;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo abwere yense wa mtima waluso mwa inu, napange zonse zimene Yehova anauza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 “Anthu onse aluso pakati panupa abwere, ndipo apange zonse zimene Chauta adalamula.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 “Anthu onse aluso pakati panu abwere ndi kupanga zonse zimene Yehova walamula:

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 35:10
6 Mawu Ofanana  

Ndipo ulankhule ndi onse a mtima waluso, amene ndawadzaza ndi mzimu waluso, kuti amsokere Aroni zovala apatulidwe nazo, andichitire Ine ntchito ya nsembe.


ndi miyala yasohamu, ndi miyala yoika ya efodi, ndi ya chapachifuwa.


Potero anatsiriza ntchito yonse ya Kachisi wa chihema chokomanako; ndipo ana a Israele adachita monga mwa zonse Yehova adamuuza Mose, anachita momwemo.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa