Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 35:11 - Buku Lopatulika

11 chihema, ndi chophimba chake, zokowera zake, ndi matabwa ake, mitanda yake, mizati, nsanamira, ndi nsichi zake, ndi makamwa ao;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Kachisi, hema wake, ndi chophimba chake, zokowera zake, ndi matabwa ake, mitanda yake, mizati, nsanamira, ndi nsichi zake, ndi makamwa ao;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Apange chihema cha Chauta, hema lake pamodzi ndi chophimbira chake, ngoŵe zake zokoŵera, mafulemu ake, mitanda yake, nsanamira zake pamodzi ndi masinde ake omwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Chihema ndi tenti yake ndiponso chophimba chake, ngowe zake, maferemu ake, mitanda yake, mizati yake ndi matsinde ake;

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 35:11
3 Mawu Ofanana  

Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa