Eksodo 35:8 - Buku Lopatulika8 ndi mafuta akuunikira, ndi zonunkhira za mafuta odzoza, ndi chofukiza cha fungo lokoma; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 ndi mafuta akuunikira, ndi zonunkhira za mafuta odzoza, ndi chofukiza cha fungo lokoma; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 mafuta anyale, zonunkhira zopangira mafuta odzozera, ndiponso zopangira lubani wonunkhira bwino, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 mafuta anyale a olivi, zonunkhiritsa mafuta odzozera ndi zopangira lubani wonunkhira; Onani mutuwo |