Eksodo 35:7 - Buku Lopatulika7 ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 chikopa chankhosa chonyika mu utoto wofiira, zikopa zambuzi, matabwa a mtengo wa kasiya, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 zikopa za nkhosa zazimuna za utoto wofiira ndi zikopa za akatumbu; matabwa amtengo wa mkesha, Onani mutuwo |