Eksodo 15:4 - Buku Lopatulika Magaleta a Farao ndi nkhondo yake anawaponya m'nyanja; ndi akazembe ake osankhika anamira mu Nyanja Yofiira. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Magaleta a Farao ndi nkhondo yake anawaponya m'nyanja; ndi akazembe ake osankhika anamira m'Nyanja Yofiira. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Chauta adaponya m'nyanja magaleta a Farao pamodzi ndi gulu lake lankhondo, adammizira atsogoleri ake amphamvu m'Nyanja Yofiira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Magaleta a Farao ndi asilikali ake ankhondo Iye wawaponya mʼnyanja. Akatswiri ankhondo amphamvu a Farao amizidwa mʼNyanja Yofiira. |
Ndipo Miriyamu anawayankha, Imbirani Yehova, pakuti wapambanatu; kavalo ndi wokwera wake anawaponya m'nyanja.