Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 15:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Magaleta a Farao ndi asilikali ake ankhondo Iye wawaponya mʼnyanja. Akatswiri ankhondo amphamvu a Farao amizidwa mʼNyanja Yofiira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Magaleta a Farao ndi nkhondo yake anawaponya m'nyanja; ndi akazembe ake osankhika anamira mu Nyanja Yofiira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Magaleta a Farao ndi nkhondo yake anawaponya m'nyanja; ndi akazembe ake osankhika anamira m'Nyanja Yofiira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 “Chauta adaponya m'nyanja magaleta a Farao pamodzi ndi gulu lake lankhondo, adammizira atsogoleri ake amphamvu m'Nyanja Yofiira.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 15:4
5 Mawu Ofanana  

Inu nokha ndiye muyenera kuopedwa. Angathe kuyima pamaso panu ndani mukakwiya?


Miriamu anawayimbira nyimbo iyi: “Imbirani Yehova, chifukwa iye wapambana. Kavalo ndi wokwerapo wake Iye wawamiza mʼnyanja.”


ndi iwe ndimaphwanya kavalo ndi wokwerapo, ndi iwe ndimaphwanya galeta ndi woyendetsa wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa