2 Samueli 3:5 - Buku Lopatulika ndi wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa Egila mkazi wa Davide. Awa anambadwira Davide ku Hebroni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa Egila mkazi wa Davide. Awa anambadwira Davide ku Hebroni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo mwana wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, wobadwa kwa Egila. Ameneŵa ndiwo ana a Davide amene adabadwira ku Hebroni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, amayi ake anali Egila, mkazi wa Davide. Ana awa a Davide anabadwira ku Hebroni. |
Ndipo panali, pokhala nkhondo pakati pa nyumba ya Saulo ndi nyumba ya Davide, Abinere analimbikira nyumba ya Saulo.