2 Samueli 3:4 - Buku Lopatulika4 ndi wachinai Adoniya mwana wa Hagiti; ndi wachisanu Sefatiya mwana wa Abitala; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndi wachinai Adoniya mwana wa Hagiti; ndi wachisanu Sefatiya mwana wa Abitala; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Wachinai anali Adoniya, wobadwa kwa Hagiti. Wachisanu anali Sefatiya wobadwa kwa Abitala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 wachinayi anali Adoniya, amayi ake anali Hagiti; wachisanu, Sefatiya amayi ake anali Abitali; Onani mutuwo |