2 Samueli 3:5 - Buku Lopatulika5 ndi wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa Egila mkazi wa Davide. Awa anambadwira Davide ku Hebroni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndi wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa Egila mkazi wa Davide. Awa anambadwira Davide ku Hebroni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ndipo mwana wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, wobadwa kwa Egila. Ameneŵa ndiwo ana a Davide amene adabadwira ku Hebroni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 ndipo wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, amayi ake anali Egila, mkazi wa Davide. Ana awa a Davide anabadwira ku Hebroni. Onani mutuwo |