Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 3:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 ndipo wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, amayi ake anali Egila, mkazi wa Davide. Ana awa a Davide anabadwira ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 ndi wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa Egila mkazi wa Davide. Awa anambadwira Davide ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 ndi wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa Egila mkazi wa Davide. Awa anambadwira Davide ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ndipo mwana wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, wobadwa kwa Egila. Ameneŵa ndiwo ana a Davide amene adabadwira ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 3:5
4 Mawu Ofanana  

wachinayi anali Adoniya, amayi ake anali Hagiti; wachisanu, Sefatiya amayi ake anali Abitali;


Pamene kunali nkhondo pakati pa banja la Sauli ndi banja la Davide, Abineri anayamba kudzipatsa yekha mphamvu pakati pa banja la Sauli.


wachisanu anali Sefatiya, amayi ake anali Abitali; wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, amayi ake anali Egila.


Ana ndiye cholowa chochokera kwa Yehova, ana ndi mphotho yochokera kwa Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa