1 Mbiri 3:3 - Buku Lopatulika3 wachisanu Sefatiya wa Abitala, wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa mkazi wake Egila. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 wachisanu Sefatiya wa Abitala, wachisanu ndi chimodzi Itireamu wa mkazi wake Egila. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mwana wake wachisanu ndi Sefatiya, mai wake anali Abitala. Mwana wake wachisanu ndi chimodzi ndi Itireamu, mai wake anali Egila. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 wachisanu anali Sefatiya, amayi ake anali Abitali; wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, amayi ake anali Egila. Onani mutuwo |