1 Mbiri 3:4 - Buku Lopatulika4 Anambadwira asanu ndi mmodzi mu Hebroni; ndi pomwepo anakhala mfumu zaka zisanu ndi ziwiri, ndi miyezi isanu ndi iwiri; ndi mu Yerusalemu anakhala mfumu zaka makumi atatu mphambu zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Anambadwira asanu ndi mmodzi m'Hebroni; ndi pomwepo anakhala mfumu zaka zisanu ndi ziwiri, ndi miyezi isanu ndi iwiri; ndi m'Yerusalemu anakhala mfumu zaka makumi atatu mphambu zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ana asanu ndi mmodzi onseŵa adabadwira ku Hebroni, kumene adakhala mfumu pa zaka zisanu ndi ziŵiri ndi miyezi isanu ndi umodzi. Koma adakhala mfumu ku Yerusalemu zaka 33. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ana asanu ndi mmodzi awa a Davide anabadwira ku Hebroni kumene analamulirako zaka zisanu ndi ziwiri ndi miyezi isanu ndi umodzi. Davide analamuliranso mu Yerusalemu kwa zaka 33, Onani mutuwo |