1 Samueli 9:17 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Samuele anaona Saulo, Yehova anati kwa iye, Ona munthu amene ndinakuuza za iye! Ameneyu adzaweruza anthu anga.
Onani mutuwo
Ndipo pamene Samuele anaona Saulo, Yehova anati kwa iye, Ona munthu amene ndinakuuza za iye! Ameneyu adzaweruza anthu anga.
Onani mutuwo
Samuele ataona Saulo, Chauta adamuuza kuti, “Ndi ameneyu munthu ndidakuuza uja. Ndiye amene adzalamulire anthu anga.”
Onani mutuwo
Samueli atamuona Sauli, Yehova anamuwuza kuti, “Munthu ndinakuwuza uja ndi uyu. Iyeyu adzalamulira anthu anga.”
Onani mutuwo