1 Samueli 9:18 - Buku Lopatulika18 Pomwepo Saulo anayandikira kwa Samuele pakati pa chipata, nati, Mundidziwitse nyumba ya mlauliyo ili kuti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pomwepo Saulo anayandikira kwa Samuele pakati pa chipata, nati, Mundidziwitse nyumba ya mlauliyo ili kuti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono Saulo adayandikira Samueleyo ku chipata namufunsa kuti, “Zikomo, kodi kunyumba kwa mlosi nkuti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Tsono Sauli anayandikira Samueli pa chipata ndipo anamufunsa, “Kodi mungandiwuze kumene kuli nyumba ya mlosi?” Onani mutuwo |