1 Samueli 9:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo Samuele anayankha Saulo nati, Ine ndine mlauliyo. Kwera, batsogola kumsanje, pakuti mudzadya ndi ine lero; ndipo m'mawa ndidzakulola upite, ndi kukudziwitsa zonse zili mumtima mwako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Samuele anayankha Saulo nati, Ine ndine mlauliyo. Kwera, batsogola kumsanje, pakuti mudzadya ndi ine lero; ndipo m'mawa ndidzakulola upite, ndi kukudziwitsa zonse zili mumtima mwako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Samuele adamuyankha kuti, “Mlosiyo ndine. Tsogolaniko ku kachisi, poti lero mudya nane, ndipo m'maŵa ndikuuzani zonse zimene zili mumtima mwanu, kenaka ndidzakulolani kuti mupite. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Samueli anayankha, “Ine ndine mlosiyo. Tsogolani kupita ku phiri pakuti lero mudya ndi ine, ndipo mawa mmawa ndidzakuwuzani zonse zimene zili mu mtima mwanu. Onani mutuwo |