Masalimo 99:2 - Buku Lopatulika2 Yehova ndiye wamkulu mu Ziyoni; ndipo akwezeka pamwamba pa mitundu yonse ya anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Yehova ndiye wamkulu m'Ziyoni; ndipo akwezeka pamwamba pa mitundu yonse ya anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Chauta ndi wamkulu ku Ziyoni. Ali pamwamba pa mitundu yonse ya anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mʼziyoni wamkulu ndi Yehova; Iye ndi wokwezeka pamwamba pa mitundu yonse ya anthu. Onani mutuwo |