Masalimo 99:1 - Buku Lopatulika1 Yehova ndiye mfumu; mitundu ya anthu injenjemere; Iye akhala pakati pa akerubi; dziko lapansi ligwedezeke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Yehova ndiye mfumu; mitundu ya anthu injenjemere; Iye akhala pakati pa akerubi; dziko lapansi ligwedezeke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta ndiye mfumu, mitundu ya anthu injenjemere. Wakhala pa akerubi ngati pa mpando wake wachifumu. Dziko lapansi ligwedezeke! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova akulamulira, mitundu ya anthu injenjemere; Iye wakhala pa mpando wake waufumu, pakati pa akerubi, dziko lapansi ligwedezeke. Onani mutuwo |
Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, pano mpokhala mpando wachifumu wanga, mpoponda kumapazi anga, pomwe ndidzakhala pakati pa ana a Israele kosatha; ndi nyumba ya Israele siidzadetsanso dzina langa loyera, ngakhale iwo kapena mafumu ao, mwa chigololo chao, ndi mitembo ya mafumu ao pa misanje yao,