Masalimo 92:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti, taonani, adani anu, Yehova, pakuti, taonani, adani anu adzatayika; ochita zopanda pake onse adzamwazika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti, taonani, adani anu, Yehova, pakuti, taonani, adani anu adzatayika; ochita zopanda pake onse adzamwazika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndithudi adani anu, Inu Chauta, adani anu adzaonongeka, onse ochita zoipa adzamwazikana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Zoonadi adani anu Yehova, zoonadi adani anu adzawonongeka; onse ochita zoyipa adzabalalitsidwa. Onani mutuwo |