Masalimo 92:10 - Buku Lopatulika10 Koma munakweza nyanga yanga ngati ya njati; anandidzoza mafuta atsopano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma munakweza nyanga yanga ngati ya njati; anandidzoza mafuta atsopano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Koma ine mwandilimbitsa ngati njati. Mwandidzoza ndi mafuta atsopano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Inu mwakweza nyanga yanga ngati nyanga ya njati; mafuta abwino akhuthulidwa pamutu wanga. Onani mutuwo |