Masalimo 92:11 - Buku Lopatulika11 Diso langa lapenya chokhumba ine pa iwo ondilalira, m'makutu mwanga ndamva chokhumba ine pa iwo akuchita zoipa akundiukira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Diso langa lapenya chokhumba ine pa iwo ondilalira, m'makutu mwanga ndamva chokhumba ine pa iwo akuchita zoipa akundiukira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Maso anga aona kuwonongeka kwa adani anga, makutu anga amva za kugwa kwa adani ondiwukira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Maso anga aona kugonjetsedwa kwa olimbana nane, makutu anga amva za kugwa kwa amaliwongo anga oyipa. Onani mutuwo |