Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 92:8 - Buku Lopatulika

8 Koma Inu, Yehova, muli m'mwamba kunthawi yonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Koma Inu, Yehova, muli m'mwamba kunthawi yonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Inu nokha Chauta, ndinu Wopambanazonse mpaka muyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Koma Inu Yehova, ndinu wokwezedwa kwamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 92:8
13 Mawu Ofanana  

Koma iwo akupatula kutsata njira zao zokhotakhota, Yehova adzawachotsa pamodzi ndi ochita zopanda pake. Mtendere ukhale pa Israele.


Pakuti adzawamweta msanga monga udzu, ndipo adzafota monga msipu wauwisi.


Adani anga afuna kundimeza tsiku lonse, pakuti ambiri andithira nkhondo modzikuza.


mpaka ndinalowa m'zoyera za Mulungu, ndi kulingalira chitsiriziro chao.


Indedi muwaika poterera, muwagwetsa kuti muwaononge.


Kuti adziwe kuti inu nokha, dzina lanu ndinu Yehova, ndinu Wam'mwambamwamba padziko lonse lapansi.


Yehova Wam'mwamba ndiye wamphamvu, wakuposa mkokomo wa madzi ambiri, ndi mafunde olimba a nyanja.


Tsopano ndidziwa kuti Yehova ali wamkulu ndi milungu yonse, pakuti momwe anadzikuza okha momwemo anawaposa.


Ukaona anthu alikutsendereza aumphawi, ndi kuchotsa chilungamo ndi chiweruzo mwachiwawa pa dera lina la dziko, usazizwepo; pakuti mkulu wopambana asamalira; ndipo alipo akulu ena oposa amenewo.


Koma nyengo imeneyo Herode mfumu anathira manja ena a mu Mpingo kuwachitira zoipa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa