Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 92:4 - Buku Lopatulika

4 Popeza Inu, Yehova, munandikondweretsa ndi kuchita kwanu, ndidzafuula mokondwera pa ntchito ya manja anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Popeza Inu, Yehova, munandikondweretsa ndi kuchita kwanu, ndidzafuula mokondwera pa ntchito ya manja anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Inu Chauta, mwandisangalatsa ndi ntchito zanu. Motero ndikufuula ndi chimwemwe chifukwa cha zimene Inu mwachita.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Pakuti Inu mumandisangalatsa ndi ntchito zanu, Inu Yehova; Ine ndikuyimba mwachimwemwe pa ntchito ya manja anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 92:4
20 Mawu Ofanana  

Ulemerero wa Yehova ukhale kosatha; Yehova akondwere mu ntchito zake;


Pomlingirira Iye pandikonde; ndidzakondwera mwa Yehova.


Yehova anatichitira ife zazikulu; potero tikhala okondwera.


Ndikumbukira masiku a kale lomwe; zija mudazichita ndilingirirapo; ndikamba pandekha za ntchito ya manja anu.


Yamikani Yehova ndi zeze; muimbireni ndi chisakasa cha zingwe khumi.


Wolungama adzakondwera mwa Yehova, nadzakhulupirira Iye; ndipo oongoka mtima onse adzalemekeza.


Munamchititsa ufumu pa ntchito za manja anu; mudagonjetsa zonse pansi pa mapazi ake;


Chochita Inu chioneke kwa atumiki anu, ndi ulemerero wanu pa ana ao.


Pakuti Yehova atero, Imbirani Yakobo ndi kukondwa, fuulirani mtundu woposawo; lalikirani, yamikirani, ndi kuti, Yehova, mupulumutse anthu anu, ndi otsala a Israele.


ndipo mzimu wanga wakondwera mwa Mulungu Mpulumutsi wanga,


Ndipo inu tsono muli nacho chisoni tsopano lino, koma ndidzakuonaninso, ndipo mtima wanu udzakondwera, ndipo palibe wina adzachotsa kwa inu chimwemwe chanu.


Koma ayamikike Mulungu, amene atitsogolera m'chigonjetso mwa Khristu, namveketsa fungo la chidziwitso chake mwa ife pamalo ponse.


Kondwera pa iye, m'mwamba iwe, ndi oyera mtima, ndi atumwi, ndi aneneri inu; chifukwa Mulungu anauweruzira kuweruzidwa kwanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa