Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 67:3 - Buku Lopatulika

3 Anthu akuyamikeni, Mulungu; anthu onse akuyamikeni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Anthu akuyamikeni, Mulungu; anthu onse akuyamikeni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Mitundu ya anthu ikutamandeni Inu Mulungu, mitundu yonse ya anthu ikuyamikeni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Mitundu ya anthu ikutamandeni Inu Mulungu; mitundu yonse ya anthu ikutamandeni.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 67:3
8 Mawu Ofanana  

Mzimu wanga ukhale ndi moyo, ndipo udzakulemekezani; ndipo maweruzo anu andithandize.


Tulutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu; olungama adzandizinga; pakuti mudzandichitira zokoma.


Ndidzawakumbutsa dzina lanu m'mibadwomibadwo; chifukwa chake mitundu ya anthu idzayamika Inu kunthawi za nthawi.


Anthu akuyamikeni, Mulungu; anthu onse akuyamikeni.


Okhalira mphanthi asabwere nao manyazi; wozunzika ndi waumphawi alemekeze dzina lanu.


inde, ati, Chili chinthu chopepuka ndithu kuti Iwe ukhale mtumiki wanga wakuutsa mafuko a Yakobo, ndi kubwezera osungika a Israele; ndidzakupatsanso ukhale kuunika kwa amitundu, kuti ukhale chipulumutso changa mpaka ku malekezero a dziko lapansi.


Chifukwa chake Iye adzawapereka kufikira nthawi yoti wobalayo wabala; pamenepo otsala a abale ake adzabwera pamodzi ndi ana a Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa