Masalimo 67:4 - Buku Lopatulika4 Anthu akondwere, nafuule mokondwera; pakuti mudzaweruza anthu molunjika, ndipo mudzalangiza anthu padziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Anthu akondwere, nafuule mokondwera; pakuti mudzaweruza anthu molunjika, ndipo mudzalangiza anthu pa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kuimba ndi chimwemwe, chifukwa Inu mumaweruza anthu mwachilungamo, ndi kuŵatsogolera pa dziko lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mitundu yonse ya anthu isangalale ndi kuyimba mwachimwemwe, pakuti inu mumaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo ndi kutsogolera mitundu ya anthu a dziko lapansi. Onani mutuwo |