Masalimo 67:5 - Buku Lopatulika5 Anthu akuyamikeni, Mulungu; anthu onse akuyamikeni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Anthu akuyamikeni, Mulungu; anthu onse akuyamikeni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mitundu yonse ya anthu ikutamandeni Inu Mulungu, mitundu yonse ya anthu ikuyamikeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mitundu ya anthu ikutamandeni Inu Mulungu; mitundu yonse ya anthu ikutamandeni. Onani mutuwo |