Masalimo 67:6 - Buku Lopatulika6 Dziko lapansi lapereka zipatso zake, Mulungu, Mulungu wathu adzatidalitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Dziko lapansi lapereka zipatso zake, Mulungu, Mulungu wathu adzatidalitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nthaka yabereka zipatso zake, Mulungu, Mulungu wathu watidalitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nthaka yabereka zokolola zake; tidalitseni Mulungu wathu. Onani mutuwo |