Masalimo 67:7 - Buku Lopatulika7 Mulungu adzatidalitsa; ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzamuopa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Mulungu adzatidalitsa; ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzamuopa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Inde, Mulungu watidalitsa, anthu onse a ku mathero a dziko lapansi apembedze Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mulungu atidalitse kuti pamenepo malekezero onse a dziko lapansi apembedze Iyeyo. Onani mutuwo |