Masalimo 68:1 - Buku Lopatulika1 Auke Mulungu, abalalike adani ake; iwonso akumuda athawe pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Auke Mulungu, abalalike adani ake; iwonso akumuda athawe pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mulungu adzambatuke, adani ake amwazikane. Onse amene amamuda, athaŵe pamaso pake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Adzuke Mulungu, adani ake amwazikane; adani ake athawe pamaso pake. Onani mutuwo |