Masalimo 68:2 - Buku Lopatulika2 Muwachotse monga utsi uchotseka; monga phula lisungunuka pamoto, aonongeke oipa pamaso pa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Muwachotse monga utsi uchotseka; monga phula lisungunuka pamoto, aonongeke oipa pamaso pa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Amwazeni iwowo monga m'mene mphepo imachitira utsi. Anthu oipa aonongeke pamaso pa Mulungu, monga m'mene sera amasungunukira pa moto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Monga momwe mphepo imachotsera utsi; Inu muwawulutsire kutali. Monga phula limasungunukira pa moto, oyipa awonongeke pamaso pa Mulungu. Onani mutuwo |