Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 6:7 - Buku Lopatulika

7 Lapuwala diso langa chifukwa cha chisoni; lakalamba chifukwa cha onse akundisautsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Lapuwala diso langa chifukwa cha chisoni; lakalamba chifukwa cha onse akundisautsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Maso anga atupa chifukwa cha kulira, afooka chifukwa cha adani anga onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Maso anga atupa chifukwa cha chisoni; akulephera kuona chifukwa cha adani anga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 6:7
10 Mawu Ofanana  

Mukumbukire Yehova kuti ndinayendabe pamaso panu m'choonadi, ndi mtima wangwiro, ndi kuchita zokoma m'kuona kwanu. Nalira Hezekiya kulira kwakukulu.


M'diso mwanga muchita chizirezire chifukwa cha chisoni, ndi ziwalo zanga zonse zilibe chithunzi.


momwemo anandilowetsa miyezi yopanda pake. Nandiikiratu zowawa usiku ndi usiku.


Pamene ndinakhala chete mafupa anga anakalamba ndi kubuula kwanga tsiku lonse.


Mtima wanga ugundagunda, mphamvu yanga yachoka, ndipo kuunika kwa maso anga, ndi iko komwe kwandichokera.


Ondida kopanda chifukwa achuluka koposa tsitsi la pamutu panga; ofuna kunditha, ndiwo adani anga monama, ali ndi mphamvu. Pamenepo andibwezetsa chosafunkha ine.


Diso langa lapuwala chifukwa cha kuzunzika kwanga: Ndimaitana Inu, Yehova, tsiku lonse; nditambalitsira manja anga kwa Inu.


Munati, Kalanga ine tsopano! Pakuti Yehova waonjezera chisoni pa zowawa zanga; ndalema ndi kubuula kwanga, sindipeza kupuma.


Chifukwa cha ichi mtima wathu ufooka, chifukwa cha izi maso athu achita chimbuuzi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa