Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 6:5 - Buku Lopatulika

5 Pakuti muimfa m'mosakumbukira Inu; m'mandamo adzakuyamikani ndani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Pakuti muimfa m'mosakumbukira Inu; m'mandamo adzakuyamikani ndani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Anthu akufa sangathe kukutamandani ku manda. M'dziko la akufa ndani angathe kukuyamikani?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Palibe amene amakukumbukirani pamene wamwalira; Amakutamandani ndani ali ku manda?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 6:5
9 Mawu Ofanana  

Akufa salemekeza Yehova, kapena aliyense wakutsikira kuli chete:


Pamenepo ndinaitana dzina la Yehova; ndikuti, Yehova ndikupemphani landitsani moyo wanga.


Sindidzafa koma ndidzakhala ndi moyo, ndipo ndidzafotokozera ntchito za Yehova.


M'mwazi mwanga muli phindu lanji, potsikira ine kudzenje? Ngati fumbi lidzayamika Inu? Ngati lidzalalikira choonadi chanu?


Bwerani, Yehova; kufikira liti? Ndipo alekeni atumiki anu.


Chilichonse dzanja lako lichipeza kuchichita, uchichite ndi mphamvu yako; pakuti mulibe ntchito ngakhale kulingirira ngakhale kudziwa, ngakhale nzeru, kumanda ulikupitako.


Tiyenera kugwira ntchito za Iye wondituma Ine, pokhala pali msana; ukudza usiku pamene palibe munthu angakhoze kugwira ntchito.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa