Masalimo 6:4 - Buku Lopatulika4 Bwererani Yehova, landitsani moyo wanga; ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Bwererani Yehova, landitsani moyo wanga; ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Bwerani, Inu Chauta, mudzandilanditse. Mundipulumutse chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Tembenukani Inu Yehova, ndipo mundilanditse; pulumutseni chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika. Onani mutuwo |