Masalimo 4:4 - Buku Lopatulika4 Chitani chinthenthe, ndipo musachimwe. Nenani mumtima mwanu pakama panu, ndipo mukhale chete. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Chitani chinthenthe, ndipo musachimwe. Nenani mumtima mwanu pakama panu, ndipo mukhale chete. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Opani Mulungu, ndipo musachimwe. Mukhale phee ndipo muganize zimenezi mu mtima pamene mukugona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kwiyani koma musachimwe; pamene muli pa mabedi anu, santhulani mitima yanu ndi kukhala chete. Sela Onani mutuwo |