Masalimo 4:3 - Buku Lopatulika3 Koma dziwani kuti Yehova anadzipatulira yekha womkondayo, adzamva Yehova m'mene ndimfuulira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Koma dziwani kuti Yehova anadzipatulira yekha womkondayo, adzamva Yehova m'mene ndimfuulira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma tsono mudziŵe kuti Chauta wadzipatulira Iye yemwe anthu olungama. Chauta amamva ndikamuitana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Dziwani kuti Yehova wadziyikira padera anthu okhulupirika; Yehova adzamva pamene ndidzamuyitana. Onani mutuwo |