Masalimo 3:8 - Buku Lopatulika8 Chipulumutso ncha Yehova; dalitso lanu likhale pa anthu anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Chipulumutso ncha Yehova; dalitso lanu likhale pa anthu anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mumatipulumutsa ndinu, Inu Chauta. Madalitso anu akhale pa anthu anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Chipulumutso chimachokera kwa Yehova. Madalitso akhale pa anthu anu. Sela Onani mutuwo |