Masalimo 3:6 - Buku Lopatulika6 Sindidzaopa unyinji wa anthu akundizinga ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Sindidzaopa unyinji wa anthu akundizinga ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Sindichita mantha ngakhale adani anga ndi osaŵerengeka, ngakhale andizinge ndi kundithira nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Sindidzaopa adani anga osawerengeka amene abwera kulimbana nane kuchokera ku madera onse. Onani mutuwo |