Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 3:5 - Buku Lopatulika

5 Ndinagona ine pansi, ndinagona tulo; ndinauka; pakuti Yehova anandichirikiza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndinagona ine pansi, ndinagona tulo; ndinauka; pakuti Yehova anandichirikiza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ndimagona ndipo ndimapeza tulo. Ndimadzukanso m'maŵa pakuti Chauta amanditchinjiriza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ine ndimagona ndi kupeza tulo; ndimadzukanso chifukwa Yehova amandichirikiza.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 3:5
11 Mawu Ofanana  

Kuli chabe kwa inu kulawirira mamawa ndi kusagonerapo madzulo, kudya mkate wosautsa kuupeza; kuli tero kuti izi apatsa okondedwa ake ngati m'tulo.


Iwo anayang'ana Iye nasanguluka; ndipo pankhope pao sipadzachita manyazi.


Ndi mtendere ndidzagona pansi, pomwepo ndidzagona tulo; chifukwa Inu, Yehova, mundikhalitsa ine, ndikhale bwino.


Iye amene asunga moyo wathu tingafe, osalola phazi lathu literereke.


Wakuopa Yehova akhulupirira kolimba; ndipo ana ake adzakhala ndi pothawirapo.


Dzina la Yehova ndilo nsanja yolimba; wolungama athamangiramo napulumuka.


Ukagona, sudzachita mantha; udzagona tulo tokondweretsa.


Inu mudzasunga mtima wokhazikika mu mtendere weniweni, chifukwa ukukhulupirirani Inu.


Ndipo ndidzapatsa mtendere m'dzikomo, kuti mudzagone pansi, wopanda wina wakukuopsani; ndidzaletsanso zilombo zisakhale m'dzikomo, lupanga lomwe silidzapita m'dziko mwanu.


Ndipo pamene Herode anati amtulutse, usiku womwewo Petro analikugona pakati pa asilikali awiri, womangidwa ndi maunyolo awiri; ndipo alonda akukhala pakhomo anadikira ndende.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa