Masalimo 2:8 - Buku Lopatulika8 Undifunse, ndipo ndidzakupatsa amitundu akhale cholowa chako, ndi malekezero a dziko lapansi akhale akoako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Undifunse, ndipo ndidzakupatsa amitundu akhale cholowa chako, ndi malekezero a dziko lapansi akhale akoako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tandipempha uwone, ndidzasandutsadi mitundu ya anthu kuti ikhale choloŵa chako, ndipo dziko lonse lapansi lidzakhala lako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tandipempha, ndipo ndidzachititsa kuti mitundu ya anthu ikhale cholowa chako; malekezero a dziko lapansi kuti akhale chuma chako. Onani mutuwo |